Numeri 33:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 “Lankhula ndi Aisiraeli, uwauze kuti, ‘Tsopano muwoloka Yorodano kuti mulowe mʼdziko la Kanani.+