Numeri 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Malirewo akafike ku Zifironi, mpaka kukathera ku Hazara-enani.+ Malire anu a mbali yakumpoto akakhale amenewa.
9 Malirewo akafike ku Zifironi, mpaka kukathera ku Hazara-enani.+ Malire anu a mbali yakumpoto akakhale amenewa.