Numeri 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Malirewo akatsike kuchokera ku Sefamu kulowera ku Ribila, kumʼmawa kwa Aini. Akatsikebe mpaka akadutse pamalo otsetsereka akumʼmawa kwa Nyanja ya Kinereti.*+
11 Malirewo akatsike kuchokera ku Sefamu kulowera ku Ribila, kumʼmawa kwa Aini. Akatsikebe mpaka akadutse pamalo otsetsereka akumʼmawa kwa Nyanja ya Kinereti.*+