Numeri 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Malo odyetserako ziweto a mizinda imene mukapereke kwa Aleviwo, akakhale mamita 445* kuchokera pampanda wa mzindawo kuzungulira mzinda wonse.
4 Malo odyetserako ziweto a mizinda imene mukapereke kwa Aleviwo, akakhale mamita 445* kuchokera pampanda wa mzindawo kuzungulira mzinda wonse.