-
Numeri 35:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mukayeze kunja kwa mzinda, mamita 890 kumbali yakumʼmawa, mamita 890 kumbali yakumʼmwera, mamita 890 kumbali yakumadzulo, ndi mamita 890 kumbali yakumpoto, kuzungulira mzinda. Amenewa akakhale malo odyetserako ziweto kwa anthu amʼmizindayo.
-