Numeri 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mizindayo ikakhale malo amene munthu wopha mnzake, amene akuthawa wobwezera magazi+ azikathawirako, kuti amene wapha mnzakeyo asaphedwe mpaka mlandu wake utaweruzidwa pamaso pa oweruza.+
12 Mizindayo ikakhale malo amene munthu wopha mnzake, amene akuthawa wobwezera magazi+ azikathawirako, kuti amene wapha mnzakeyo asaphedwe mpaka mlandu wake utaweruzidwa pamaso pa oweruza.+