-
Numeri 35:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Wobwezera magazi ndi amene ayenera kupha munthu amene wapha mnzakeyo. Akadzangomupeza, wobwezera magaziyo adzamuphe.
-