-
Numeri 35:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 kapenanso wafa wina atamumenya ndi dzanja lake chifukwa chodana naye, amene wapha mnzakeyo aphedwe ndithu. Iye ndi wopha munthu. Wobwezera magazi aphe wopha munthuyo akangomupeza.
-