-
Numeri 36:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Cholowa cha Aisiraeli chisamachotsedwe ku fuko lina kupita ku fuko lina. Aliyense wa Aisiraeli ayenera kusunga cholowa cha fuko la makolo ake.
-