Numeri 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amenewa ndi malamulo ndi zigamulo za Yehova, zimene anapereka kwa Aisiraeli kudzera mwa Mose ku Yeriko, mʼchipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano.+
13 Amenewa ndi malamulo ndi zigamulo za Yehova, zimene anapereka kwa Aisiraeli kudzera mwa Mose ku Yeriko, mʼchipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano.+