-
Deuteronomo 1:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
1 Awa ndi mawu amene Mose analankhula ndi Aisiraeli onse mʼchipululu, mʼchigawo cha Yorodano, mʼchigwa chimene chinali moyangʼanizana ndi Sufu, pakati pa Parana, Tofeli, Labani, Hazeroti ndi Dizahabi.
-