Deuteronomo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova Mulungu wa makolo anu achulukitse chiwerengero chanu+ kuwirikiza maulendo 1,000, ndipo akudalitseni mogwirizana ndi zimene anakulonjezani.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:11 Nsanja ya Olonda,3/1/1988, ptsa. 18-19
11 Yehova Mulungu wa makolo anu achulukitse chiwerengero chanu+ kuwirikiza maulendo 1,000, ndipo akudalitseni mogwirizana ndi zimene anakulonjezani.+