Deuteronomo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musamakondere poweruza mlandu.+ Munthu wamba ndi munthu wolemekezeka, onse muziwamvetsera chimodzimodzi.+ Musamaope anthu+ chifukwa mukuweruzira Mulungu+ ndipo ngati mlandu wakuvutani muzibwera nawo kwa ine kuti ndiumve.’+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:17 Nsanja ya Olonda,9/15/2004, tsa. 257/1/1992, tsa. 17
17 Musamakondere poweruza mlandu.+ Munthu wamba ndi munthu wolemekezeka, onse muziwamvetsera chimodzimodzi.+ Musamaope anthu+ chifukwa mukuweruzira Mulungu+ ndipo ngati mlandu wakuvutani muzibwera nawo kwa ine kuti ndiumve.’+