Deuteronomo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma nonse munabwera kwa ine nʼkundiuza kuti, ‘Tiyeni titumize amuna kuti akatifufuzire zokhudza dzikolo ndipo adzatiuze njira imene tikuyenera kudzera ndiponso mizinda imene tikaipeze kumeneko.’+
22 Koma nonse munabwera kwa ine nʼkundiuza kuti, ‘Tiyeni titumize amuna kuti akatifufuzire zokhudza dzikolo ndipo adzatiuze njira imene tikuyenera kudzera ndiponso mizinda imene tikaipeze kumeneko.’+