Deuteronomo 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iwo anatengako zina mwa zipatso zamʼdzikolo nʼkutibweretsera, ndipo anatiuza kuti, ‘Dziko limene Yehova Mulungu wathu akufuna kutipatsa ndi labwino.’+
25 Iwo anatengako zina mwa zipatso zamʼdzikolo nʼkutibweretsera, ndipo anatiuza kuti, ‘Dziko limene Yehova Mulungu wathu akufuna kutipatsa ndi labwino.’+