Deuteronomo 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma inu munakana kupita kukalowa mʼdzikolo, ndipo munapandukira lamulo la Yehova Mulungu wanu.+