-
Deuteronomo 1:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Choncho munapitiriza kungʼungʼudza mʼmatenti anu kuti, ‘Yehova anatitulutsa mʼdziko la Iguputo chifukwa choti ankadana nafe, ndipo akufuna kutipereka mʼmanja mwa Aamori kuti atiwononge.
-