Deuteronomo 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova Mulungu wanu adzakutsogolerani ndipo adzakumenyerani nkhondo,+ ngati mmene anachitira ku Iguputo inu mukuona.+
30 Yehova Mulungu wanu adzakutsogolerani ndipo adzakumenyerani nkhondo,+ ngati mmene anachitira ku Iguputo inu mukuona.+