Deuteronomo 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 amene ankayenda patsogolo panu kuti akufufuzireni malo oti mumangepo msasa. Usiku ankakutsogolerani ndi moto ndipo masana ankakutsogolerani ndi mtambo kuti akusonyezeni njira yoti muyendemo.+
33 amene ankayenda patsogolo panu kuti akufufuzireni malo oti mumangepo msasa. Usiku ankakutsogolerani ndi moto ndipo masana ankakutsogolerani ndi mtambo kuti akusonyezeni njira yoti muyendemo.+