Deuteronomo 1:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nthawi yonseyi Yehova ankamva zimene munkanena ndipo anakwiya kwambiri, moti analumbira kuti,+