-
Deuteronomo 1:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Choncho ine ndinalankhula nanu, koma inu simunamvere. Mʼmalomwake, munapandukira lamulo la Yehova nʼkuchita zinthu modzikuza, moti munanyamuka kupita mʼphirimo.
-