Deuteronomo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani pa chilichonse chimene mukuchita. Iye akudziwa bwino kuti mukuyenda mʼchipululu chachikuluchi. Yehova Mulungu wanu wakhala nanu zaka 40 zimenezi, ndipo simunasowe kanthu.”’+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:7 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2022, ptsa. 5-6
7 Chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani pa chilichonse chimene mukuchita. Iye akudziwa bwino kuti mukuyenda mʼchipululu chachikuluchi. Yehova Mulungu wanu wakhala nanu zaka 40 zimenezi, ndipo simunasowe kanthu.”’+