Deuteronomo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho tinadutsa pafupi ndi abale athu, mbadwa za Esau,+ amene akukhala ku Seiri, ndipo sitinayende njira ya Araba, Elati ndi Ezioni-geberi.+ Kenako tinatembenuka nʼkudutsa njira ya mʼchipululu cha Mowabu.+
8 Choncho tinadutsa pafupi ndi abale athu, mbadwa za Esau,+ amene akukhala ku Seiri, ndipo sitinayende njira ya Araba, Elati ndi Ezioni-geberi.+ Kenako tinatembenuka nʼkudutsa njira ya mʼchipululu cha Mowabu.+