Deuteronomo 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu amenewa anali amphamvu kwambiri komanso ochuluka ndipo anali ataliatali ngati Aanaki.+ Koma Yehova anawagonjetsa pamaso pa Aamoni, ndipo Aamoniwo anawathamangitsa moti anatenga dzikolo nʼkumakhalamo.
21 Anthu amenewa anali amphamvu kwambiri komanso ochuluka ndipo anali ataliatali ngati Aanaki.+ Koma Yehova anawagonjetsa pamaso pa Aamoni, ndipo Aamoniwo anawathamangitsa moti anatenga dzikolo nʼkumakhalamo.