-
Deuteronomo 2:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 mpaka kukawoloka Yorodano nʼkulowa mʼdziko limene Yehova Mulungu wathu anatipatsa. Izi nʼzimene mbadwa za Esau zimene zikukhala ku Seiri komanso Amowabu amene akukhala ku Ari anandichitira.’
-