Deuteronomo 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma simunayandikire dziko la Aamoni,+ dera lonse lamʼmbali mwa chigwa cha Yaboki,*+ kapena mizinda yamʼdera lamapiri, kapenanso malo alionse amene Yehova Mulungu wathu anatiletsa.”
37 Koma simunayandikire dziko la Aamoni,+ dera lonse lamʼmbali mwa chigwa cha Yaboki,*+ kapena mizinda yamʼdera lamapiri, kapenanso malo alionse amene Yehova Mulungu wathu anatiletsa.”