Deuteronomo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawi imeneyo tinalanda dziko la mafumu awiri a Aamori+ amene ankakhala mʼdera la Yorodano, kuyambira mʼchigwa cha Arinoni* mpaka kuphiri la Herimoni.+
8 Pa nthawi imeneyo tinalanda dziko la mafumu awiri a Aamori+ amene ankakhala mʼdera la Yorodano, kuyambira mʼchigwa cha Arinoni* mpaka kuphiri la Herimoni.+