Deuteronomo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa nthawi imeneyo ndinakulamulani kuti: ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna onse olimba mtima atenge zida ndipo awoloke patsogolo pa abale anu, Aisiraeli.+
18 Pa nthawi imeneyo ndinakulamulani kuti: ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna onse olimba mtima atenge zida ndipo awoloke patsogolo pa abale anu, Aisiraeli.+