Deuteronomo 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma Yehova anapitiriza kundikwiyira chifukwa cha inu,+ ndipo sanandimvere. Mʼmalomwake Yehova anandiuza kuti, ‘Basi khala chete! Usadzandiuzenso nkhani imeneyi.
26 Koma Yehova anapitiriza kundikwiyira chifukwa cha inu,+ ndipo sanandimvere. Mʼmalomwake Yehova anandiuza kuti, ‘Basi khala chete! Usadzandiuzenso nkhani imeneyi.