Deuteronomo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pajatu Yehova Mulungu wathu amayankha mapemphero athu nthawi zonse. Kodi pali mtundu winanso wamphamvu umene milungu yake ili nawo pafupi chonchi?+
7 Pajatu Yehova Mulungu wathu amayankha mapemphero athu nthawi zonse. Kodi pali mtundu winanso wamphamvu umene milungu yake ili nawo pafupi chonchi?+