-
Deuteronomo 4:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Pa nthawi imeneyo Yehova anandilamula kuti ndikuphunzitseni malangizo ndi zigamulo, zimene mukuyenera kukazitsatira mukakalowa mʼdziko limene mukukalitenga kuti likhale lanu.
-