Deuteronomo 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anandikwiyira chifukwa cha inu,+ ndipo analumbira kuti sadzandilola kuti ndiwoloke Yorodano kapena kupita mʼdziko labwino limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale cholowa chanu.+
21 Yehova anandikwiyira chifukwa cha inu,+ ndipo analumbira kuti sadzandilola kuti ndiwoloke Yorodano kapena kupita mʼdziko labwino limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale cholowa chanu.+