Deuteronomo 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ineyo ndifera mʼdziko lino. Sindiwoloka Yorodano,+ koma inu muwoloka nʼkukatenga dziko labwinoli.