Deuteronomo 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Samalani kuti musaiwale pangano la Yehova Mulungu wanu limene anachita ndi inu+ ndipo musapange chifaniziro chosema, chifaniziro cha chinthu chilichonse chimene Yehova Mulungu wanu anakuletsani.+
23 Samalani kuti musaiwale pangano la Yehova Mulungu wanu limene anachita ndi inu+ ndipo musapange chifaniziro chosema, chifaniziro cha chinthu chilichonse chimene Yehova Mulungu wanu anakuletsani.+