Deuteronomo 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mukakakhala ndi ana komanso zidzukulu ndipo mukakakhala nthawi yaitali mʼdzikomo, nʼkuchita zinthu zokuwonongetsani popanga chifaniziro chosema+ cha chinthu chilichonse, nʼkuchita choipa pamaso pa Yehova Mulungu wanu, moti nʼkumukhumudwitsa,+
25 Mukakakhala ndi ana komanso zidzukulu ndipo mukakakhala nthawi yaitali mʼdzikomo, nʼkuchita zinthu zokuwonongetsani popanga chifaniziro chosema+ cha chinthu chilichonse, nʼkuchita choipa pamaso pa Yehova Mulungu wanu, moti nʼkumukhumudwitsa,+