Deuteronomo 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kumeneko mudzatumikira milungu yamtengo ndi mwala, yopangidwa ndi manja a anthu,+ milungu imene singaone, kumva, kudya kapena kununkhiza.
28 Kumeneko mudzatumikira milungu yamtengo ndi mwala, yopangidwa ndi manja a anthu,+ milungu imene singaone, kumva, kudya kapena kununkhiza.