-
Deuteronomo 4:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Tafunsani tsopano, za masiku akale inu musanakhalepo, kuchokera pa tsiku limene Mulungu analenga munthu padziko lapansi. Mufufuze kuchokera kumalekezero a thambo kukafika kumalekezero ena a thambo. Kodi zinthu zazikulu ngati zimenezi zinayamba zachitikapo, kapena kodi pali amene anamvapo zinthu ngati zimenezi?+
-