Deuteronomo 4:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anakuchititsani kuti mumve mawu ake kuchokera kumwamba nʼcholinga chakuti akulangizeni kuti muzimumvera. Padziko lapansi pano, iye anakuchititsani kuti muone moto waukulu, ndipo munamva mawu ake kuchokera pamotowo.+
36 Anakuchititsani kuti mumve mawu ake kuchokera kumwamba nʼcholinga chakuti akulangizeni kuti muzimumvera. Padziko lapansi pano, iye anakuchititsani kuti muone moto waukulu, ndipo munamva mawu ake kuchokera pamotowo.+