Deuteronomo 4:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho mudziwe lero, ndipo muzikumbukira mumtima mwanu kuti Yehova ndi Mulungu woona, kumwamba ndiponso padziko lapansi.+ Palibenso wina.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:39 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 4
39 Choncho mudziwe lero, ndipo muzikumbukira mumtima mwanu kuti Yehova ndi Mulungu woona, kumwamba ndiponso padziko lapansi.+ Palibenso wina.+