Deuteronomo 4:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Pa nthawi imeneyo, Mose anapatula mizinda itatu mbali yakumʼmawa kwa Yorodano.+