Deuteronomo 4:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Iwo anamulanda dziko lakelo komanso dziko la Ogi+ mfumu ya Basana. Amenewa ndi mafumu awiri a Aamori amene anali kuchigawo chakumʼmawa kwa Yorodano.
47 Iwo anamulanda dziko lakelo komanso dziko la Ogi+ mfumu ya Basana. Amenewa ndi mafumu awiri a Aamori amene anali kuchigawo chakumʼmawa kwa Yorodano.