Deuteronomo 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno munati, ‘Yehova Mulungu wathu watisonyeza ulemerero wake ndi ukulu wake, ndipo tamva mawu ake kuchokera mʼmoto.+ Lero taona kuti Mulungu angalankhule ndi munthu, munthuyo nʼkukhalabe ndi moyo.+
24 Ndiyeno munati, ‘Yehova Mulungu wathu watisonyeza ulemerero wake ndi ukulu wake, ndipo tamva mawu ake kuchokera mʼmoto.+ Lero taona kuti Mulungu angalankhule ndi munthu, munthuyo nʼkukhalabe ndi moyo.+