-
Deuteronomo 5:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Kodi pali munthu aliyense amene anamvapo mawu a Mulungu wamoyo, akulankhula kuchokera mʼmoto ngati mmene ife tachitiramu nʼkukhalabe ndi moyo?
-