Deuteronomo 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iweyo upite pafupi ukamvetsere zonse zimene Yehova Mulungu wathu akanene. Ndiyeno iweyo udzatiuze zonse zimene Yehova Mulungu wathu wakuuza, ndipo ife tidzamvera nʼkuchita zomwezo.’+
27 Iweyo upite pafupi ukamvetsere zonse zimene Yehova Mulungu wathu akanene. Ndiyeno iweyo udzatiuze zonse zimene Yehova Mulungu wathu wakuuza, ndipo ife tidzamvera nʼkuchita zomwezo.’+