-
Deuteronomo 5:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Koma iwe ukhale pompano, ndipo ndikuuza malamulo onse, malangizo ndi zigamulo zimene ukuyenera kuwaphunzitsa kuti azikazitsatira mʼdziko limene ndikuwapatsa kuti likhale lawo.’
-