Deuteronomo 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 mukasamale kuti musakaiwale Yehova+ amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo, mʼnyumba yaukapolo.