Deuteronomo 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 chifukwa Yehova Mulungu wanu amene ali pakati panu ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.+ Mukatsatira milungu ina, mkwiyo wa Yehova Mulungu wanu udzakuyakirani+ ndipo adzakufafanizani padziko lapansi.+
15 chifukwa Yehova Mulungu wanu amene ali pakati panu ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.+ Mukatsatira milungu ina, mkwiyo wa Yehova Mulungu wanu udzakuyakirani+ ndipo adzakufafanizani padziko lapansi.+