-
Deuteronomo 6:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Muzionetsetsa kuti mukusunga malamulo a Yehova Mulungu wanu, zikumbutso zake ndi malangizo ake amene wakulamulani kuti muziwatsatira.
-