Deuteronomo 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muzichita zoyenera ndi zabwino pamaso pa Yehova kuti zikuyendereni bwino komanso kuti mukalowe mʼdziko labwino limene Yehova analumbira kwa makolo anu, nʼkulitenga kuti likhale lanu,+
18 Muzichita zoyenera ndi zabwino pamaso pa Yehova kuti zikuyendereni bwino komanso kuti mukalowe mʼdziko labwino limene Yehova analumbira kwa makolo anu, nʼkulitenga kuti likhale lanu,+