Deuteronomo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musadzachite nawo mgwirizano uliwonse wa ukwati.* Musadzapereke ana anu aakazi kwa ana awo aamuna ndipo musadzatenge ana awo aakazi nʼkuwapereka kwa ana anu aamuna.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:3 Nsanja ya Olonda,11/1/1989, ptsa. 20-21
3 Musadzachite nawo mgwirizano uliwonse wa ukwati.* Musadzapereke ana anu aakazi kwa ana awo aamuna ndipo musadzatenge ana awo aakazi nʼkuwapereka kwa ana anu aamuna.+